Ma team a PSG komaso Arsenal akukumana muma semi-finals mumpikisano wa UEFA Champions League. PSG ikutsogola ndi chigoli chimodzi kutengela kupambana kwawo (1-0) mumasewelo oyamba amu semi-final pa Emirates stadium.