Artists
Zomwe Zayaka
Congratulations Driemo
Driemo wakhala oyimba oyamba kumalawi kulandila youtube play button award.

Driemo wapanga mbili pokhala oyimba oyamba ku Malawi kulandila youtube play button award. Iyi ndi award yomwe imapatsidwa kwaanthu amene ma channel awo afika 100,000 subscribers. Kupatulapo kufika 100,000 subscribers omwe amalandila award iyiyi amayenela kukhala kuti samapalamula ku youtube.
Congratulations Driemo
#Bitse Media
#Olivia Media


