Gospel
Thupi lake linali Labwinobwino koma linasintha kukhala lachi alubino
Eeee nkhani iyi ndiyokhidza kwambili 😢😢
Anali munthu wakuda bwinobwino ndipo amagwila ntchito yomanga koma pano anasiya chifukwa achipatala anawaiza kuti asiye kugwila ntchito za hard komas asamakhale padzuwa. Thupi lawo linasintha kukhala lachi kwa chaka chimodzi.



