Videos
Akatero Namadingo waledzera
People are saying Dr. Namadingo is sounding drunk in this video – koma kodi ndi zoona kapena anthu akungofuna nkhani?
Tione limodzi momwe video iyi yalimbikitsira zokambirana pa social media.
Onani bwino, muweruze nokha ndipo tipezeni m’magawo a ndemanga kuti mutiuze maganizo anu.