Alfred Gangata anayankhula pansonkhano wina kuti anthu amene anapangila campaign DPP akuyenela apindule, ndipo ena anakhumudwa nawo kuti samayenela kuyankhula choncho pokhalaso nduna. Koma mayi awa ayankhula mogwilizana ndia Gangata kuti anavutika okha kupanga campaign.
#bitse_Media #Oliviamedia



