Sports
Zomwe Zayaka
Masapota kufuna kumenyana mu minbus itatha game ya Silver Strikers ndi Mighty Wanderers
Anthu anafuna kugwilana mthupi pamene amatsutsana zasewelo apakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers omwe anathela 2-2. Anthuwa amatsutsana maka pazakuimbila kwa Referee pomwe anakana chigoli cha Wanderes komaso zakupeleka Penalty ku Silver Strikers. Nkhani yonse ili mu video iyi.



