Gossip
Zomwe Zayaka
ABWEZI MWANDIONA AKUDANDAULANI AMALAWI
Abwezi mwandiona abwela kudzayankha atanenedwa pa social media
Atanenedwa ndi anthu ambili pa social media Kamba kamaloto amene akuti amafuna amuuze Eli Njuchi abwezi abwela kudzafotokoza kuti mwawaweluza musanave zomwe amafuna kunena bwanji?


