Gossip
Zomwe Zayaka
Alice Andrews Wamusambwadza Virginia wa Abwezi Mwandiwona pankhani yolota Eli njuchi
Chakatu chothaitha zikuchitika izi
Kucha kwa dzulo Abwezi mwandiona adzuka mkuti alota maloto ndipo akufunitsitsa amuuze Eli njuchi. Koma Alice atava zimenezi sanaugwile ayi koma kumuthila mphepo.


