NewsPolitics
Zomwe Zayaka

Otsutsa Boma ayiwale zolowaso m’boma

Anthu akupitilizabe kupeleka maganizo awo payemwe akuyenela kukhala president pachisankho chapa 16 September 2025

Anthu ma minbus akupitizabe kupeleka maganizo awo payemwe akuyenela kusankhidwa ngati mtsogoleri wadziko pazisankho zikubwelazi. Mfundo zomwe zikumatukuka ndimonga

  • Chakwela walephela
  • Opposition ilibe mphavu
  • Apitilize chakwela yemweyo.

Inu maganizo anu ndiotan.

Related Articles

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Back to top button