Videos
Prophet Shepherd Bushiri vs Steven Kayuni
Steven Kayuni ali pa mpanipani pomwe Bushiri wanenetsa kuti mwana wake anatisiya chifukwa cha
chipongwe chomwe anachita mkuluyi ndipo nkhani apapa itelera sayendera kuti iye ndi man of God
ai koma athethetsana ndi Kayuni mpaka akathere ku waya.
Bushiri akuti anafa ng’ombe ndipo pokhapa anamva kuwawa kwambiri. Ngakhale anakhululuka koma
chilungamo chiyende ngati shot ya gin kukhosi kwa chidakwa.
Kupuma kulibe ku Malawi 




