News

ZIMAYI UYU ANATHETSA BANJA CHIFUKWA CHA IZI?

Banja linathera Ku honeymoon chifukwa mamunayo ali ndi chimbunju! (from inbox)
__________
Hello Olivia Media. ine dzina langa ndi Judith ndipo ine ndi mamuna wanga takhala pachibwezi Kwa zaka 5 ndipo masiku ena timasinjana moveka bwino muja ndipo ine nkumayamika kuti mamuna Wana amanditha ludzu

Koma chomwe chinachitika tisanakwatirane ndichomwe chinandipangitsa kuti ndithetsee banja. nkhani yonse ili motere;

Ine ndi boyfriend wanga tinagwilizana kuti tikwatirane mu chaka cha 2024 Choncho pankafunika ndalama ya za ukwati komaso kuti tiyambe business yodalilika, Choncho tinagwilizana kuti mamuna wangayo apite Ku South Africa kukathama for one year kenako azikabwera , ndipo izi zinachitikadi muchaka cha 2023 march ndipo asananyamuke timasinjana ma round 4 tonse nkuvetsaso.

Mwamwayi atafika Ku SA sanachedwe kupeza ntchito yabwinoo ndipo akamandiuza pa phone Amati amamulipira bwino kwambiri. Patapita miyezi 6 ndinanabwa mamuna wanga uja atayamba kuchepetsa Moto machedwe anthu apa WhatsApp and I knew kuti something is wrong.. komabe pena ndimadzilimbitsa mtima kumati mamuna wanga sangandichite chipongwe.

Patatha miyezi ina itatu ndinadabwa kuti boyfriend wanga sakupezekaso online kufikira Feb 2024 pomwe ndinalandira phone pa new number ya chimalawi ndipo mau ndinawazindikira kuti ndi boyfriend wanga uja , inetu sinachedwee koma kufusa kuti wafikira kuti, kuti ndikamulandire mwantundu uli wonse boyfriend wanga.

Nditapita room yomwe anafikira hotel ina Ku lilongwe ine ndinali wodabwa kuwona boyfriend wanga akukana k!ss or kusinjana, kumufusa why? iye anagoti “izizi tiyeni tisiye Kaye”….. ine sanamee ndinakozekera ma style amtundu Onse patsikuli poti tinasowana koma ndinangoti it’s okay

Fast forward nthawi imapita ndipo pressure ya ukwati inayamba kubwera kuchokera Kwa makoro, ndipo posachedwa date linakozedwa and boyfriend wanga tikati tishowane amagoti aayi tidikire tikwatirane (koma I missed him badly 😢)

Tsiku laukwati linafika ndipo zonse zinachitika , inali nthawi ya Ku honeymoon, tili Ku room boyfriend wanga amawuma wuma kuti avure zovala koma ine nkuti nyer* itandivuta kwambiri coz nkuti nditatha chaka osadyedwakoo 😢 ine ndinakakamira kumuvura, koma sadly ine ndinaona mamuna wanga alibe gada Pali seeeee( chinatsara ndi chimbinjuu ) , ine sinavetseee ndipo nditamufusa kuti chinakuchitikira ndichani Iweee 🙄? ndipamene amafotokoza kuti Ali Ku South Africa kuja anamugwira Ali ndi Mkazi wamwini ndee anangomudula basi eeeeh sanamee I was in shock

After two days ine ndinagomuza kuti this marriage can’t work ….mpaka I filed for divorce

Eti nkumati apa ndinalakwitsa ?

Related Articles

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Back to top button