News
-
ABWEZI MWANDIONA AKUDANDAULANI AMALAWI
Atanenedwa ndi anthu ambili pa social media Kamba kamaloto amene akuti amafuna amuuze Eli Njuchi abwezi abwela kudzafotokoza kuti mwawaweluza…
Read More » -
-
Alice Andrews Wamusambwadza Virginia wa Abwezi Mwandiwona pankhani yolota Eli njuchi
Kucha kwa dzulo Abwezi mwandiona adzuka mkuti alota maloto ndipo akufunitsitsa amuuze Eli njuchi. Koma Alice atava zimenezi sanaugwile ayi…
Read More » -
Anthu Ambili amaifuna Program Ya Hot Current akachoka M’boma
achina Brian Banda ndi azake akuti anthu ambili amaifuna program ya hot current akachoka m’boma.
Read More » -
Masapota kufuna kumenyana mu minbus itatha game ya Silver Strikers ndi Mighty Wanderers
Anthu anafuna kugwilana mthupi pamene amatsutsana zasewelo apakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers omwe anathela 2-2. Anthuwa amatsutsana maka…
Read More » -
Mpungwepungwe ku chipani cha MCP
Ku chipani cha MCP kuli mpungwepungwe paza amene akhale leader of opposition kunyumba yamalamulo
Read More » -
ZIMAYI UYU ANATHETSA BANJA CHIFUKWA CHA IZI?
Banja linathera Ku honeymoon chifukwa mamunayo ali ndi chimbunju! (from inbox) __________ Hello Olivia Media. ine dzina langa ndi Judith…
Read More » -
-
Evance Meleka wakana zoti wamenyedwa
Mmodzi mwa oyimba nyimbo zauzimu, Evance Watsopano Meleka, watsutsa mpheketsera zomwe ena akufalitsa pa masamba a mchezo kuti uye wamenyedwa.…
Read More » -
Suleman kufotoza za mulandu wake ndi Jessie Kabwila omwe uli ku khothi
Iyiyi izathela mapenate ndithuπ π π π
Read More »